Salimo 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+ Mlaliki 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ineyo ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Ine ndili ndi nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso mtima wanga wapeza nzeru zambiri ndiponso wadziwa zinthu zambiri.”+ Mlaliki 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mulungu woona adzaweruza munthu wolungama ndi munthu woipa,+ pakuti iye ali ndi nthawi yochitira chinthu chilichonse ndiponso yokhudza ntchito iliyonse.”+
2 Ndi amene akuyenda mosalakwitsa zinthu,+ amene amachita chilungamo,+Ndi kulankhula zoona mumtima mwake.+
16 Ineyo ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Ine ndili ndi nzeru zambiri kuposa aliyense amene anakhalapo mu Yerusalemu ine ndisanakhalepo.+ Komanso mtima wanga wapeza nzeru zambiri ndiponso wadziwa zinthu zambiri.”+
17 Ine ndinanena mumtima mwanga+ kuti: “Mulungu woona adzaweruza munthu wolungama ndi munthu woipa,+ pakuti iye ali ndi nthawi yochitira chinthu chilichonse ndiponso yokhudza ntchito iliyonse.”+