Yeremiya 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndinaona mapiri ndipo anali kugwedezeka. Zitunda zonse zinali kunjenjemera.+ Nahumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+ Habakuku 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anaima chilili kuti agwedeze dziko lapansi.+ Anayang’ana mitundu ya anthu ndipo mitunduyo inadumpha.+ Mapiri amuyaya anaphwanyidwa.+ Zitunda zimene zidzakhalapo mpaka kalekale* zinawerama.+ Zimenezi ndi njira zake zakalekale.
5 Mapiri agwedezeka chifukwa cha iye ndipo zitunda zasungunuka.+ Dziko lapansi, nthaka ndi zinthu zonse zokhala m’dzikomo zidzanjenjemera.+
6 Iye anaima chilili kuti agwedeze dziko lapansi.+ Anayang’ana mitundu ya anthu ndipo mitunduyo inadumpha.+ Mapiri amuyaya anaphwanyidwa.+ Zitunda zimene zidzakhalapo mpaka kalekale* zinawerama.+ Zimenezi ndi njira zake zakalekale.