Yobu 21:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kodi iwo amakhala ngati udzu wouluzika ndi mphepo?+Kapena ngati mankhusu* ouluka ndi mphepo yamkuntho? Salimo 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma oipa sali choncho.Iwo ali ngati mankhusu* amene amauluzika ndi mphepo.+ Salimo 35:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Akhale ngati mankhusu ouluzika ndi mphepo,+Mngelo wa Yehova awapitikitse.+ Yesaya 17:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mitundu ya anthu+ idzasokosera ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula,+ ndipo iwo adzathawira kutali. Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo m’mapiri ndiponso adzauluzika ngati tizitsotso touluzika ndi mphepo yamkuntho.+
18 Kodi iwo amakhala ngati udzu wouluzika ndi mphepo?+Kapena ngati mankhusu* ouluka ndi mphepo yamkuntho?
13 Mitundu ya anthu+ idzasokosera ngati mkokomo wa madzi ambiri. Iye adzawadzudzula,+ ndipo iwo adzathawira kutali. Adzathamangitsidwa ngati mankhusu* ouluzika ndi mphepo m’mapiri ndiponso adzauluzika ngati tizitsotso touluzika ndi mphepo yamkuntho.+