Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete. Levitiko 22:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Musaipitse dzina langa loyera,+ m’malomwake muzindiona kukhala wopatulika pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+ Mateyu 6:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Koma inu muzipemphera motere:+ “‘Atate wathu wakumwamba, dzina+ lanu liyeretsedwe.+
3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.
32 Musaipitse dzina langa loyera,+ m’malomwake muzindiona kukhala wopatulika pakati pa ana a Isiraeli.+ Ine ndine Yehova amene ndikukupatulani kuti mukhale oyera.+