Levitiko 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete. Yesaya 29:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 pakuti akaona ana ake pakati pake, ntchito ya manja anga,+ iwo adzayeretsa dzina langa.+ Adzayeretsadi Woyera wa Yakobo,+ ndipo adzalemekeza kwambiri Mulungu wa Isiraeli.+ Luka 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pamenepo iye anawauza kuti: “Mukamapemphera+ muzinena kuti, ‘Atate, dzina lanu liyeretsedwe.+ Ufumu wanu ubwere.+
3 Chotero Mose anauza Aroni kuti: “Yehova wanena kuti, ‘Anthu amene ali pafupi ndi ine+ ayenera kundiona kukhala woyera,+ ndipo anthu onse azindipatsa ulemerero.’”+ Pamenepo Aroni anangokhala chete.
23 pakuti akaona ana ake pakati pake, ntchito ya manja anga,+ iwo adzayeretsa dzina langa.+ Adzayeretsadi Woyera wa Yakobo,+ ndipo adzalemekeza kwambiri Mulungu wa Isiraeli.+
2 Pamenepo iye anawauza kuti: “Mukamapemphera+ muzinena kuti, ‘Atate, dzina lanu liyeretsedwe.+ Ufumu wanu ubwere.+