Levitiko 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe+ kwa Moleki.*+ Usanyoze+ dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi. Ine ndine Yehova.+ Levitiko 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Musamalumbire zabodza m’dzina langa+ ndi kuipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova. Amosi 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+
21 “‘Usalole kuti aliyense mwa ana ako aperekedwe+ kwa Moleki.*+ Usanyoze+ dzina la Mulungu wako mwa njira imeneyi. Ine ndine Yehova.+
7 Iwo akufunitsitsa kuti fumbi la padziko lapansi ligwere pamitu ya anthu wamba+ ndipo sakuchitira chilungamo anthu ofatsa.+ Mwana pamodzi ndi bambo ake akugona ndi mtsikana mmodzi+ ndi cholinga chofuna kuipitsa dzina langa loyera.+