Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 32:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Panthaka ya anthu anga, pakungomera zitsamba zaminga.+ Zamera panyumba zonse zimene kale zinali zodzaza ndi chisangalalo. Zamera m’tauni imene kale inali yodzaza ndi chikondwerero.+

  • Hoseya 9:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Inutu mudzachoka chifukwa dzikolo lidzasakazidwa.+ Anthu a ku Iguputo adzakusonkhanitsani pamodzi+ ndipo anthu a ku Mofi+ adzakuikani m’manda. Zomera zoyabwa zidzamera pakatundu wanu wabwino wasiliva.+ M’mahema mwanu mudzamera zitsamba zaminga.+

  • Zefaniya 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Yehova wa makamu, Mulungu wa Isiraeli wanena kuti: “Pali ine Mulungu wamoyo,+ Mowabu adzakhala ndendende ngati Sodomu,+ ndipo ana a Amoni+ adzakhala ngati Gomora, malo odzaza zomera zoyabwa ndiponso mchere ndiponso malo abwinja mpaka kalekale.*+ Otsala mwa anthu anga adzafunkha zinthu zawo, ndipo otsala a mtundu wa anthu anga adzawagwira ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena