Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 72:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Padziko lapansi padzakhala tirigu wambiri.+

      Pamwamba pa mapiri padzakhala tirigu wochuluka.+

      Zokolola za mfumu zidzachuluka ngati mitengo ya ku Lebanoni,+

      Ndipo anthu ochokera mumzinda adzaphuka ngati udzu wa panthaka.+

  • Yesaya 60:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 “Ulemerero wa Lebanoni udzabwera kwa iwe. Mtengo wofanana ndi mkungudza, mtengo wa ashi, ndiponso mtengo wa paini zidzabwera pa nthawi imodzi,+ kuti zikongoletse malo anga opatulika,+ ndipo ine ndidzalemekeza malo oikapo mapazi anga.+

  • Yesaya 61:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 ndiponso kuti anthu onse amene akulirira Ziyoni ndiwapatse nsalu yovala kumutu m’malo mwa phulusa,+ ndiwapatse mafuta kuti azisangalala+ m’malo molira, ndiwapatse chovala choti azivala ponditamanda m’malo mokhala otaya mtima.+ Iwo adzatchedwa mitengo ikuluikulu ya chilungamo,+ yobzalidwa ndi Yehova+ kuti iyeyo akongole.+

  • Hoseya 14:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Nthambi zake zidzaphukira ndipo adzakhala ndi ulemerero ngati mtengo wa maolivi.+ Fungo lake lonunkhira lidzakhala ngati mtengo wa ku Lebanoni.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena