13 Kodi simukudziwa zimene ineyo ndi makolo anga tinachita kwa anthu onse a mayiko ena?+ Kodi milungu+ ya mitundu ya mayiko ena inatha kupulumutsa mayiko awo m’manja mwanga?
11 kodi sizidzachitika kuti monga momwe ndidzachitire kwa Samariya ndi kwa milungu yake yopanda phindu,+ ndi mmenenso ndidzachitire kwa Yerusalemu ndi kwa mafano ake?’+
18 Musamvere Hezekiya chifukwa akukunyengererani+ ndi mawu akuti, ‘Yehova atilanditsa.’ Kodi pali mulungu wa mitundu ina amene wakwanitsa kupulumutsa mtundu wake m’manja mwa mfumu ya Asuri?+