Yesaya 32:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+ Yesaya 55:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+ Yesaya 60:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+
15 kufikira mzimu utatsanulidwa pa ife kuchokera kumwamba,+ ndiponso chipululu chitakhala munda wa zipatso. Munda wa zipatsowo udzakhala ngati nkhalango yeniyeni.+
13 M’malo mwa chitsamba chaminga padzamera mtengo wa mkungudza.+ M’malo mwa chomera choyabwa padzamera mtengo wa mchisu.+ Zimenezi zidzamutchukitsa Yehova,+ ndipo zidzakhala chizindikiro choti sichidzachotsedwa mpaka kalekale.”+
21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+