Yobu 38:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+ Yesaya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+ Mika 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+
3 Takokera chovala chako n’kuchimanga m’chiuno ngati mwamuna wamphamvu.Ndikufuna ndikufunse mafunso ndipo iweyo undiyankhe.+
8 Amene adzanene kuti ndine wolungama ali pafupi.+ Ndani angalimbane nane? Tiyeni tikaonane pabwalo lamilandu.+ Kodi wotsutsana nane pa mlandu ndani?+ Abwere kufupi.+
2 Inu mapiri, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake. Inu matanthwe okhazikika, tamverani. Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+ pakuti Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake. Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+