Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 29:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 pakuti akaona ana ake pakati pake, ntchito ya manja anga,+ iwo adzayeretsa dzina langa.+ Adzayeretsadi Woyera wa Yakobo,+ ndipo adzalemekeza kwambiri Mulungu wa Isiraeli.+

  • Yesaya 60:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Anthu ako onse adzakhala olungama.+ Iwo adzakhala m’dzikomo mpaka kalekale.+ Anthuwo adzakhala mmera wobzalidwa ndi ine+ ndiponso ntchito ya manja anga,+ kuti ineyo ndikongoletsedwe.+

  • Yeremiya 3:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ine ndanena kuti, ‘Mokondwera ndinakuikani pakati pa ana anga ndi kukupatsani dziko labwino,+ cholowa chimene mitundu yambiri ya anthu imachisirira!’ Ndipo ndinanenanso kuti, ‘Anthu inu mudzandiitana kuti, “Atate wanga!”+ ndipo mudzandilondola osabwerera.’

  • Hoseya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Ndiyeno ana a Isiraeli adzachuluka ngati mchenga wakunyanja umene munthu sangathe kuuyeza kapena kuuwerenga.+ Ndipo kumene anali kuuzidwa kuti, ‘Anthu inu sindinu anthu anga,’+ adzauzidwanso kuti, ‘Inu ndinu ana a Mulungu wamoyo.’+

  • Agalatiya 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena