Yeremiya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka. Nahumu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yehova wa makamu wanena kuti: “Taona! Ine ndikukuukira,+ ndipo ndidzakuvula siketi yako ndi kukuphimba nayo kumaso moti ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ione maliseche ako+ ndi kutinso maufumu aone manyazi ako.
22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka.
5 Yehova wa makamu wanena kuti: “Taona! Ine ndikukuukira,+ ndipo ndidzakuvula siketi yako ndi kukuphimba nayo kumaso moti ndidzachititsa kuti mitundu ya anthu ione maliseche ako+ ndi kutinso maufumu aone manyazi ako.