Yesaya 47:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tenga mphero+ upere ufa. Vula nsalu yako yophimba kumutu.+ Vula chovala chako chokhwekhwerera pansi.+ Ukweze chovala chako m’mwamba mpaka miyendo ionekere,+ ndipo uwoloke mitsinje. Yeremiya 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka. Ezekieli 16:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+ Chivumbulutso 17:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Nyanga 10+ waziona zija, komanso chilombo,+ zimenezi zidzadana nalo hulelo.+ Zidzalisakaza ndi kulisiya lamaliseche. Zidzadya minofu yake ndi kulinyeketsa ndi moto.+
2 Tenga mphero+ upere ufa. Vula nsalu yako yophimba kumutu.+ Vula chovala chako chokhwekhwerera pansi.+ Ukweze chovala chako m’mwamba mpaka miyendo ionekere,+ ndipo uwoloke mitsinje.
22 Ukadzanena mumtima mwako kuti,+ ‘N’chifukwa chiyani zinthu zimenezi zandigwera?’+ pamenepo udzadziwe kuti wavulidwa siketi yako+ ndipo zidendene zako zazunzidwa chifukwa zolakwa zako zachuluka.
37 ine ndisonkhanitsa pamodzi zibwenzi zako zonse zimene unali kuzisangalatsa. Ndisonkhanitsanso anthu onse ochokera kumalo onse okuzungulira amene unali kuwakonda limodzi ndi onse amene unali kudana nawo kuti akuukire. Ndidzakuvula pamaso pawo ndipo iwo adzaona maliseche ako onse.+
16 Nyanga 10+ waziona zija, komanso chilombo,+ zimenezi zidzadana nalo hulelo.+ Zidzalisakaza ndi kulisiya lamaliseche. Zidzadya minofu yake ndi kulinyeketsa ndi moto.+