Salimo 65:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+ Yesaya 30:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munabzala munthaka,+ ndipo zokolola za munthakayo zidzakhala chakudya chopatsa thanzi.+ M’tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+
9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+Mwalilemeretsa kwambiri.Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+
23 Mulungu adzabweretsa mvula pambewu zanu zimene munabzala munthaka,+ ndipo zokolola za munthakayo zidzakhala chakudya chopatsa thanzi.+ M’tsiku limenelo, ziweto zanu zidzadya msipu pamalo aakulu odyetserapo ziweto.+