Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 11:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma dziko limene mukuwolokerako kuti mukalitenge kukhala lanu ndi dziko lamapiri ndi zigwa.+ Ilo limamwa madzi a mvula, madzi ochokera kumwamba.

  • Salimo 65:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Inu mwatembenukira dziko lapansi kuti mulipatse zinthu zochuluka,+

      Mwalilemeretsa kwambiri.

      Mtsinje wochokera kwa Mulungu ndi wosefukira ndi madzi.+

      Munalinganiza zinthu, kuti mbewu zawo zibale.+

      Umu ndi mmene mumaperekera zinthu padziko lapansi.+

  • Salimo 104:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Mulungu amathirira mapiri kuchokera m’zipinda zake za m’mwamba.+

      Dziko lapansi ladzaza ndi zipatso za ntchito yake.+

  • Zekariya 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 “Pemphani Yehova kuti akugwetsereni mvula+ pa nthawi ya mvula yomalizira.+ Pemphani Yehova amene anapanga mitambo yamvula+ ndiponso amene amagwetsera anthu mvula yamphamvu.+ Iye amapereka mbewu m’munda mwa munthu aliyense.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena