3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+
9 Pambuyo pake Zera Mwitiyopiya+ anabwera kudzamenyana nawo ali ndi gulu lankhondo la asilikali 1,000,000+ ndi magaleta 300, ndipo anafika ku Maresha.+