Yeremiya 30:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yehova wanena kuti: “Ndikusonkhanitsa anthu a m’mahema a Yakobo+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina ndipo ndidzamvera chisoni malo okhala a Yakobo. Mzinda udzamangidwanso pachiunda chake+ ndipo nsanja yokhalamo idzakhala pamalo ake oyenera.+ Yeremiya 32:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’” Amosi 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+
18 Yehova wanena kuti: “Ndikusonkhanitsa anthu a m’mahema a Yakobo+ amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina ndipo ndidzamvera chisoni malo okhala a Yakobo. Mzinda udzamangidwanso pachiunda chake+ ndipo nsanja yokhalamo idzakhala pamalo ake oyenera.+
41 Ndidzakondwera nawo ndi kuwachitira zabwino.+ Ndidzawabzala m’dziko lino+ mokhulupirika ndi mtima wanga wonse komanso ndi moyo wanga wonse.’”
11 “‘Pa tsiku limenelo, ndidzautsa+ nyumba+ ya Davide imene inagwa,+ ndi kukonza mmene khoma* lake linawonongeka. Ndidzautsa mabwinja ake ndipo ndidzaimanga kuti ikhale ngati masiku akale.+