Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 71:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Pakuti chiyembekezo changa ndinu,+ Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, ndimadalira inu kuyambira pa unyamata wanga.+

  • Miyambo 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 amene wasiya mnzake wapamtima wa pachitsikana chake+ ndiponso amene waiwala pangano limene anapangana ndi Mulungu wake.+

  • Yeremiya 2:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Pita, ukafuule m’makutu a anthu a ku Yerusalemu kuti, ‘Yehova wanena kuti:+ “Ndikukumbukira bwino kwambiri kukoma mtima kosatha kumene unali nako pamene unali wachinyamata,+ chikondi chimene unali nacho pa nthawi imene unali kulonjezedwa kukwatiwa,+ ndi kuti unanditsatira poyenda m’chipululu, m’dziko losabzalidwa kalikonse.+

  • Hoseya 2:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Kuyambira nthawi imeneyo mpaka m’tsogolo ndidzamupatsa minda yake ya mpesa.+ Ndidzamupatsanso chigwa cha Akori+ kuti chikhale ngati khomo lachiyembekezo. Pamenepo adzayankha ngati mmene anali kuyankhira ali mtsikana,+ ngatinso mmene anayankhira pa tsiku limene anatuluka m’dziko la Iguputo.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena