Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 30:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anthu a mtundu wanu obalalitsidwawo akadzakhala kumalekezero kwa thambo, Yehova Mulungu wanu adzakusonkhanitsani ndi kukutengani kumeneko.+

  • Yesaya 49:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Koma Yehova wanena kuti: “Ngakhale gulu la anthu ogwidwa ndi munthu wamphamvu lidzatengedwa,+ ndipo amene anatengedwa kale ndi wolamulira wankhanza adzathawa.+ Aliyense wolimbana nawe, ineyo ndidzalimbana naye,+ ndipo ana ako ndidzawapulumutsa.+

  • Yeremiya 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ine ndidzasonkhanitsa pamodzi nkhosa zanga zotsala kuchokera m’mayiko onse kumene ndinazibalalitsira+ ndipo ndidzazibwezeretsa kumalo awo kumene zimadyera.+ Nkhosazo zidzaberekana ndi kuchuluka.+

  • Yeremiya 30:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Pakuti, “taona! masiku adzafika,” watero Yehova, “pamene ndidzasonkhanitsa Isiraeli ndi Yuda,+ anthu anga amene anagwidwa ndi kutengedwa kupita kudziko lina,” watero Yehova. “Iwo ndidzawabwezeretsa kudziko limene ndinapatsa makolo awo ndipo adzalitenga kukhalanso lawo.”’”+

  • Ezekieli 39:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 “‘Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, ndikadzawapititsa kumayiko ena n’kuwabwezanso kudziko lawo onse pamodzi.+ Kumayikowo ndidzatengako Aisiraeli onse moti sindidzasiyako aliyense.+

  • Yoweli 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 “Ndiyeno masiku amenewo ndiponso pa nthawi imeneyo,+ ndidzabwezeretsa anthu a ku Yuda ndi a ku Yerusalemu amene anagwidwa ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena