Salimo 25:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+ Zekariya 9:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+ Maliko 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Yesu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino?+ Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+
8 Yehova ndi wabwino ndi wolungama.+N’chifukwa chake amalangiza ochimwa kuti ayende m’njira yoyenera.+
17 Ubwino wake ndi waukulu kwambiri+ ndiponso iye ndi wooneka bwino kwambiri.+ Tirigu adzapatsa mphamvu anyamata ndipo vinyo watsopano adzapatsa mphamvu anamwali.”+
18 Yesu anam’funsa kuti: “N’chifukwa chiyani ukunditchula kuti wabwino?+ Palibe wabwino, koma Mulungu yekha.+