Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Palibe anthu odzitama amene angaime pamaso panu.+

      Mumadana ndi onse ochita zopweteka ena.+

  • Yeremiya 15:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chotero Yehova wanena kuti: “Ukabwerera kwa ine, inenso ndidzakukonda,+ ndipo udzanditumikira.+ Ukasiyanitsa zinthu zamtengo wapatali ndi zinthu zopanda phindu, udzakhala ngati kamwa langa. Anthuwo adzabwera kwa iwe, koma iwe sudzapita kwa iwo.”

  • Luka 21:36
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 36 Chotero khalani maso+ ndipo muzipemphera mopembedzera+ nthawi zonse, kuti mudzathe kuthawa zinthu zonsezi zimene zikuyembekezeka kuchitika. Kutinso mudzathe kuima pamaso pa Mwana wa munthu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena