Yeremiya 37:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo akalonga+ anamukwiyira kwambiri Yeremiya+ ndipo anamumenya+ ndi kumutsekera m’ndende+ m’nyumba ya Yehonatani+ mlembi, pakuti nyumba yake ndi imene anaisandutsa ndende.+ Yeremiya 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+
15 Pamenepo akalonga+ anamukwiyira kwambiri Yeremiya+ ndipo anamumenya+ ndi kumutsekera m’ndende+ m’nyumba ya Yehonatani+ mlembi, pakuti nyumba yake ndi imene anaisandutsa ndende.+
20 Tsopano ndimvereni chonde, mbuyanga mfumu. Chonde, mverani pempho langa lakuti mundikomere mtima.+ Musandibwezere kunyumba ya Yehonatani+ mlembi, chifukwa ndingakafere kumeneko.”+