Salimo 31:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndamva zinthu zoipa zimene anthu ambiri akunena,+Ndamva zochititsa mantha kuchokera kumbali zonse.+Akasonkhana pamodzi kundichitira upo,+Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+ Yeremiya 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Musatuluke kupita kunja ndipo musayende m’njira pakuti kumeneko kuli lupanga la mdani. Zochititsa mantha zili paliponse.+ Yeremiya 46:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.
13 Ndamva zinthu zoipa zimene anthu ambiri akunena,+Ndamva zochititsa mantha kuchokera kumbali zonse.+Akasonkhana pamodzi kundichitira upo,+Amakonza chiwembu kuti achotse moyo wanga.+
25 Musatuluke kupita kunja ndipo musayende m’njira pakuti kumeneko kuli lupanga la mdani. Zochititsa mantha zili paliponse.+
5 “‘N’chifukwa chiyani akuoneka kuti agwidwa ndi mantha? Akubwerera, ndipo amuna awo amphamvu aphwanyika ndi kukhala zidutswazidutswa. Iwo athawadi ndipo sanacheuke.+ Zochititsa mantha zili paliponse,’+ watero Yehova.