Yesaya 19:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+ Ezekieli 29:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana kwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+
19 Uwu ndi uthenga wokhudza Iguputo:+ Taonani! Yehova wakwera mtambo wothamanga+ ndipo akubwera mu Iguputo. Milungu yopanda pake ya ku Iguputo idzanjenjemera chifukwa chomuopa+ ndipo mitima ya Aiguputo idzasungunuka mkati mwa dzikolo.+
2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana kwa Farao mfumu ya Iguputo+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzachitikire iyeyo ndi dziko lonse la Iguputo.+