Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako, uzitumize kwa mfumu ya Edomu,+ mfumu ya Mowabu,+ mfumu ya ana a Amoni,+ mfumu ya Turo+ ndi mfumu ya Sidoni.+ Upatsire amithenga amene akubwera ku Yerusalemu kudzaonana ndi Zedekiya mfumu ya Yuda.

  • Ezekieli 32:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 “‘Kumeneko n’kumene kuli Edomu,+ mafumu ake ndi atsogoleri ake onse. Amenewa anaikidwa m’manda akadali amphamvu. Anaikidwa pamodzi ndi ophedwa ndi lupanga.+ Iwo adzagona limodzi ndi anthu osadulidwa+ komanso anthu amene akutsikira kudzenje.

  • Obadiya 1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 1 Tsopano awa ndiwo masomphenya a Obadiya:

      Zimene Yehova Ambuye Wamkulu Koposa wanena zokhudza Edomu ndi izi:+ “Ife tamva uthenga wochokera kwa Yehova ndipo nthumwi yatumidwa kwa anthu a mitundu ina kukanena kuti: ‘Nyamukani anthu inu, tiyeni timuukire ndi kumenyana naye.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena