Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 22:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Yehova wanena kuti, ‘Ndibweretsa tsoka+ pamalo ano ndi anthu ake,+ kukwaniritsa mawu onse+ a m’buku limene mfumu ya Yuda yawerenga,+

  • 2 Mbiri 34:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 “Yehova wanena kuti, ‘Ndibweretsa tsoka+ pamalo ano ndi anthu ake,+ pokwaniritsa matemberero onse+ amene analembedwa m’buku limene anawerenga pamaso pa mfumu ya Yuda,+

  • Yeremiya 6:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Tamverani, inu okhala padziko lapansi! Ine ndikubweretsa tsoka pa anthu awa+ chifukwa cha maganizo awo,+ pakuti sanamvere mawu anga ndipo anapitirizabe kukana chilamulo changa.”+

  • Ezekieli 7:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Tsoka! Tsoka loti silinaonekepo likubwera.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena