Maliro 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Aneneri ako aona masomphenya achabechabe ndi opanda pake+ onena za iwe.Iwo sanaulule zolakwa zako kuti akuteteze n’cholinga choti usatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma anali kuona masomphenya achabechabe ndi osocheretsa+ onena za iwe. Ezekieli 12:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakati pa nyumba ya Isiraeli sipadzakhalanso masomphenya opanda pake+ kapena kulosera kwachiphamaso.+ Zekariya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+
14 Aneneri ako aona masomphenya achabechabe ndi opanda pake+ onena za iwe.Iwo sanaulule zolakwa zako kuti akuteteze n’cholinga choti usatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma anali kuona masomphenya achabechabe ndi osocheretsa+ onena za iwe.
24 Pakati pa nyumba ya Isiraeli sipadzakhalanso masomphenya opanda pake+ kapena kulosera kwachiphamaso.+
2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+