Salimo 30:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+ Yesaya 33:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+
5 Chifukwa mkwiyo wa Mulungu sukhalitsa pa munthu,+Koma kukoma mtima kwake ndi kwa moyo wonse.+Usiku kumakhala kulira,+ koma m’mawa kumakhala kufuula ndi chisangalalo.+
2 Inu Yehova, tikomereni mtima.+ Ife tikudalira inu.+ Tilimbitseni ndi dzanja lanu+ m’mawa uliwonse.+ Mukhale chipulumutso chathu pa nthawi ya masautso.+