1 Mafumu 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Anamanganso mizinda yake yonse yosungirako zinthu,+ mizinda yosungirako magaleta,+ mizinda ya amuna okwera pamahatchi, ndiponso zilizonse zimene iye anakonda+ kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni, ndi m’dziko lonse limene ankalamulira. 1 Mafumu 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+ Maliro 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.
19 Anamanganso mizinda yake yonse yosungirako zinthu,+ mizinda yosungirako magaleta,+ mizinda ya amuna okwera pamahatchi, ndiponso zilizonse zimene iye anakonda+ kumanga ku Yerusalemu, ku Lebanoni, ndi m’dziko lonse limene ankalamulira.
27 Mfumuyo inachititsa kuti ku Yerusalemu siliva akhale wochuluka kwambiri ngati miyala,+ ndiponso kuti matabwa a mkungudza akhale ochuluka kwambiri ngati mitengo yamkuyu ya ku Sefela.+
10 Mdani watambasula dzanja lake n’kutenga zinthu+ zake zonse zabwino.Yerusalemu waona mitundu ina itabwera ndi kulowa m’malo ake opatulika,+Mitundu imene munalamula kuti isalowe mumpingo wanu.