Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:66
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 66 Pamenepo moyo wako udzakhala pangozi yaikulu koopsa, ndipo udzakhala wamantha usiku ndi usana, moti sudzakhala wotsimikiza za moyo wako.+

  • Yesaya 24:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Aliyense wothawa phokoso la chinthu chochititsa mantha adzagwera m’dzenje,+ ndipo aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha. Pakuti zotsekera madzi akumwamba zidzatseguka+ ndipo maziko a dziko adzagwedezeka.+

  • Yeremiya 48:44
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 44 ‘Aliyense wothawa chifukwa cha mantha adzagwera m’dzenje. Aliyense wotuluka m’dzenjemo adzagwidwa mumsampha.’+

      “‘Pakuti ine ndidzachititsa kuti chaka chopereka chilango kwa anthu a ku Mowabu chifike,’+ watero Yehova.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena