Ezekieli 16:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 “‘Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimaperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi,+ ndipo ndidzakupatsa magazi a mkwiyo ndi nsanje.+ Ezekieli 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kuweruza?+ Kodi uweruza mzinda umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ ndi kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+
38 “‘Ndidzakupatsa chiweruzo chimene chimaperekedwa kwa akazi achigololo+ ndi kwa akazi okhetsa magazi,+ ndipo ndidzakupatsa magazi a mkwiyo ndi nsanje.+
2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kuweruza?+ Kodi uweruza mzinda umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ ndi kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+