Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 28:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nawonso Afilisiti+ anaukira mizinda ya Yuda ya ku Sefela+ ndi ku Negebu+ n’kulanda mizinda ya Beti-semesi,+ Aijaloni,+ Gederoti,+ Soko+ ndi midzi yake yozungulira, Timuna+ ndi midzi yake yozungulira, komanso Gimizo ndi midzi yake yozungulira, n’kuyamba kukhala kumeneko.

  • Yesaya 9:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Siriya adzachokera kum’mawa+ ndipo Afilisiti adzachokera kumadzulo.+ Iwo adzadya Isiraeli ndi pakamwa potsegula.+ Chifukwa cha zonsezi, mkwiyo wake sunabwerere, ndipo dzanja lake lidakali lotambasula.+

  • Yeremiya 47:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Yehova anauza mneneri Yeremiya mawu okhudza Afilisiti.+ Pa nthawiyi, Farao anali asanathire nkhondo mzinda wa Gaza.+

  • Amosi 1:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 “Yehova wanena kuti, ‘“Chifukwa chakuti Gaza wandipandukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa. Sindidzamusinthira chigamulocho chifukwa chakuti anthu onse ogwidwa ukapolo+ anawapereka ku Edomu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena