Yeremiya 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+ Ezekieli 25:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Afilisiti achitira zoipa+ Aisiraeli ndipo akupitiriza kuwachitira zoipazo. Mumtima mwawo akusangalala ndiponso kuwanyoza. Akuchita zimenezi kuti awawononge+ chifukwa cha chidani chawo chomwe chidzakhalepo mpaka kalekale.+ Zefaniya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,+ ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Kunena za Asidodi,+ anthu ake adzawathamangitsa dzuwa lili paliwombo,+ ndipo Ekironi adzazulidwa.+
20 khamu lonse la anthu a mitundu yosiyanasiyana, mafumu onse a dziko la Uzi,+ mafumu onse a dziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza,+ Ekironi+ ndi otsala onse a ku Asidodi,+
15 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Afilisiti achitira zoipa+ Aisiraeli ndipo akupitiriza kuwachitira zoipazo. Mumtima mwawo akusangalala ndiponso kuwanyoza. Akuchita zimenezi kuti awawononge+ chifukwa cha chidani chawo chomwe chidzakhalepo mpaka kalekale.+
4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,+ ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Kunena za Asidodi,+ anthu ake adzawathamangitsa dzuwa lili paliwombo,+ ndipo Ekironi adzazulidwa.+