7 Amuna a Isiraeli amene anali m’dera la m’chigwa ndiponso m’dera la Yorodano ataona kuti asilikali a Isiraeli athawa komanso kuti Sauli ndi ana ake afa, anayamba kuchoka m’mizinda yawo ndi kuthawa.+ Kenaka Afilisiti anabwera n’kuyamba kukhala m’mizindayo.+