Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamwamba pake panali aserafi.+ Mserafi aliyense anali ndi mapiko 6. Mapiko awiri anaphimbira nkhope yake,+ awiri anaphimbira mapazi ake ndipo awiri anali kuulukira.

  • Ezekieli 10:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pa zamoyo zinayizo, chamoyo chilichonse chinali ndi nkhope zinayi+ ndi mapiko anayi, ndipo kupansi kwa mapiko awo kunali zinthu zooneka ngati manja a munthu.

  • Chivumbulutso 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Zamoyo zinayizo,+ chilichonse chinali ndi mapiko 6.+ Zinali ndi maso thupi lonse ngakhalenso kunsi kwa mapiko.+ Zamoyo zimenezi sizinali kupuma usana ndi usiku. Zinali kunena kuti: “Woyera, woyera, woyera ndiye Yehova+ Mulungu, Wamphamvuyonse,+ amene analipo, amene alipo,+ ndi amene akubwera.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena