Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 “‘“Mtima wako unadzikweza chifukwa cha kukongola kwako.+ Unawononga nzeru zako chifukwa cha ulemerero wako wonyezimira.+ Ndidzakuponyera kudziko lapansi+ ndipo mafumu azidzakuyang’ana.+

  • Ezekieli 32:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndidzachititsa mantha anthu ambiri a mitundu ina chifukwa cha iwe.+ Ndikadzawaloza ndi lupanga langa kumaso,+ mafumu awo adzanjenjemera ndi mantha. Kuyambira pa tsiku limene udzaphedwe, aliyense wa iwo azidzanjenjemera nthawi zonse chifukwa choopa kufa.’+

  • Chivumbulutso 18:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Mafumu+ a dziko lapansi amene anachita naye dama ndi kusangalala ndi chuma mopanda manyazi, adzalira ndi kudziguguda pachifuwa ndi chisoni chifukwa cha iye,+ poona utsi+ wofuka chifukwa cha kupsa kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena