Danieli 11:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Mfumuyo idzachita zofuna zake ndipo idzadzikweza ndi kudzikuza kuposa mulungu aliyense.+ Iyo idzalankhula zinthu zodabwitsa zotsutsana ndi Mulungu wa milungu.+ Idzapambana kufikira chidzudzulo champhamvu chitaperekedwa chonse,+ chifukwa chinthu chimene chakonzedwa chiyenera kuchitika. 1 Akorinto 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+
36 “Mfumuyo idzachita zofuna zake ndipo idzadzikweza ndi kudzikuza kuposa mulungu aliyense.+ Iyo idzalankhula zinthu zodabwitsa zotsutsana ndi Mulungu wa milungu.+ Idzapambana kufikira chidzudzulo champhamvu chitaperekedwa chonse,+ chifukwa chinthu chimene chakonzedwa chiyenera kuchitika.
5 Pakuti ngakhale ilipo yotchedwa “milungu,”+ kaya kumwamba+ kapena padziko lapansi,+ ndipo n’zoona ilipodi “milungu” yambiri ndi “ambuye” ambiri,+