Levitiko 26:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+ Salimo 105:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iye anadzetsa njala yaikulu m’dzikomo,+Ndipo anathyola ndodo zonse zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati.+ Yesaya 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+ Ezekieli 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+
26 Ndikadzathyola ndodo zanu zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati,+ akazi 10 adzaphika mkate mu uvuni umodzi, ndipo adzakugawirani mochita kukuyezerani pamuyezo.+ Chotero mudzadya koma simudzakhuta.+
16 Iye anadzetsa njala yaikulu m’dzikomo,+Ndipo anathyola ndodo zonse zopachikapo mkate wozungulira woboola pakati.+
3 Tamverani! Ambuye woona,+ Yehova wa makamu, akuchotsa mu Yerusalemu+ ndi mu Yuda zinthu zonse zofunika pa moyo. Akuchotsa mkate, madzi,+
16 “‘Ndikadzakutumizirani mivi yakupha yobweretsa njala+ imene idzakuwonongeni,+ ndidzachititsa kuti njala ikule pakati panu, ndipo ndidzathyola ndodo zimene mumakolowekapo mikate yozungulira yoboola pakati.+