Ezekieli 20:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana+ ku mbali ya kum’mwera ndipo ulankhule+ mawu onena za kumeneko. Ulosere kunkhalango ya dziko la kum’mwera. Ezekieli 21:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+ Ezekieli 33:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Dzikolo ndidzalisandutsa bwinja+ ndiponso malo owonongeka. Ndidzathetsa mphamvu zimene dzikolo limanyadira.+ Mapiri a mu Isiraeli adzawonongedwa+ ndipo sipadzapezeka wodutsamo.
46 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana+ ku mbali ya kum’mwera ndipo ulankhule+ mawu onena za kumeneko. Ulosere kunkhalango ya dziko la kum’mwera.
2 “Iwe mwana wa munthu, yang’ana ku Yerusalemu ndipo ulankhule+ kwa malo oyera.+ Ulosere zoipa zimene zidzachitikire dziko la Isiraeli.+
28 Dzikolo ndidzalisandutsa bwinja+ ndiponso malo owonongeka. Ndidzathetsa mphamvu zimene dzikolo limanyadira.+ Mapiri a mu Isiraeli adzawonongedwa+ ndipo sipadzapezeka wodutsamo.