Yeremiya 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova. Hoseya 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pamenepo ana a Yuda ndi ana a Isiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzadziikira mtsogoleri mmodzi ndi kutuluka m’dzikolo,+ chifukwa tsikuli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.*+ Zekariya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndithu ndidzabwerera ku Yerusalemu ndi kuchitira chifundo mzinda umenewu.+ Nyumba yanga idzamangidwa mmenemo,+ ndipo chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa makamu.’
31 “Pa nthawi imeneyo ndidzakhala Mulungu wa mabanja onse a Isiraeli, ndipo iwo adzakhala anthu anga,”+ watero Yehova.
11 Pamenepo ana a Yuda ndi ana a Isiraeli adzasonkhanitsidwa pamodzi ndipo adzakhala ogwirizana.+ Iwo adzadziikira mtsogoleri mmodzi ndi kutuluka m’dzikolo,+ chifukwa tsikuli lidzakhala lofunika kwambiri kwa Yezereeli.*+
16 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘“Ndithu ndidzabwerera ku Yerusalemu ndi kuchitira chifundo mzinda umenewu.+ Nyumba yanga idzamangidwa mmenemo,+ ndipo chingwe choyezera chidzatambasulidwa pa Yerusalemu,”+ watero Yehova wa makamu.’