Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 6:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano akulu+ a Ayuda anali kupita patsogolo pa ntchito yomanga+ nyumbayo atalimbikitsidwa ndi ulosi wa mneneri Hagai+ ndi Zekariya+ mdzukulu wa Ido.+ Iwo anamanga nyumbayo ndi kuimaliza potsatira lamulo la Mulungu wa Isiraeli,+ ndi lamulo la Koresi,+ Dariyo,+ ndi Aritasasita+ mfumu ya Perisiya.

  • Yesaya 44:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Ndine amene ndikunena za Koresi+ kuti, ‘Iye ndi m’busa wanga ndipo adzakwaniritsa bwinobwino zonse zimene ndikufuna,’+ ngakhale zimene ndanena zokhudza Yerusalemu zakuti, ‘Adzamangidwanso,’ ndi zokhudza kachisi zakuti, ‘Maziko ako adzamangidwa.’”+

  • Hagai 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yehova analimbikitsa+ Zerubabele mwana wa Salatiyeli bwanamkubwa wa Yuda, Yoswa+ mwana wa Yehozadaki mkulu wa ansembe ndi anthu ena onse. Choncho iwo anapita kukagwira ntchito panyumba ya Yehova wa makamu, Mulungu wawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena