Numeri 16:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake. Deuteronomo 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+ Ezekieli 40:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Chipinda chodyeramo chimene chayang’ana kumpoto ndi cha ansembe ogwira ntchito paguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Iwo ndi ochokera mwa ana a Levi ndipo amayandikira Yehova ndi kum’tumikira.”+
5 Ndiyeno Mose analankhula ndi Kora ndiponso khamu lonselo, kuti: “Mawa m’mawa, Yehova aonetsa amene ali wake+ ndiponso amene ali woyera.+ Aonetsa amene ayenera kuima pamaso pake,+ ndipo amene ati am’sankheyo+ adzaima pamaso pake.
5 “Ansembe, ana a Levi, azifika pafupi chifukwa ndi amene Yehova Mulungu wanu wawasankha kuti am’tumikire+ ndi kudalitsa+ m’dzina la Yehova. Iwo ndiwo ayenera kuthetsa mkangano uliwonse wokhudza choipa chilichonse chimene chachitika.+
46 Chipinda chodyeramo chimene chayang’ana kumpoto ndi cha ansembe ogwira ntchito paguwa lansembe,+ omwe ndi ana a Zadoki.+ Iwo ndi ochokera mwa ana a Levi ndipo amayandikira Yehova ndi kum’tumikira.”+