Deuteronomo 31:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pakuti ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma khosi kwanu.+ Ngati lero pamene ndili moyo pamodzi nanu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova,+ ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga! Yesaya 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mukakana+ n’kupanduka, mudzawonongedwa ndi lupanga, chifukwa pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+ Yesaya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+ Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+
27 Pakuti ineyo ndikudziwa bwino khalidwe lanu lopanduka+ ndi kuuma khosi kwanu.+ Ngati lero pamene ndili moyo pamodzi nanu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova,+ ndiye kuli bwanji pambuyo pa imfa yanga!
20 Koma mukakana+ n’kupanduka, mudzawonongedwa ndi lupanga, chifukwa pakamwa pa Yehova m’pamene panena zimenezi.”+
9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+
5 Kaya iwowo akamvetsera+ kapena ayi,+ pakuti iwo ndi nyumba yopanduka,+ adzadziwabe kuti pakati pawo panali mneneri.+