Nehemiya 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikukongoza ndalama ndi chakudya kwa abale athu. Chonde, tiyeni tileke kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+ Salimo 82:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mudzaweruza mopanda chilungamo,+Ndi kukondera anthu oipa kufikira liti?+ [Seʹlah.] Yesaya 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+
10 Ndiponso ine, abale anga ndi atumiki anga, tikukongoza ndalama ndi chakudya kwa abale athu. Chonde, tiyeni tileke kulandira chiwongoladzanja tikakongoza zinthu.+
17 Phunzirani kuchita zabwino.+ Funafunani chilungamo.+ Dzudzulani munthu wopondereza ena.+ Weruzani mwachilungamo mwana wamasiye.*+ Thandizani mkazi wamasiye pa mlandu wake.”+