Ezekieli 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi n’kupita pakhomo la nyumba yopatulika, ndipo mtambo+ unadzaza nyumbayo pang’onopang’ono. Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza m’bwalo lonse la nyumbayo. Ezekieli 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako, ulemerero wa Yehova+ unakwera m’mwamba kuchoka pakati pa mzindawo, n’kukaima pamwamba pa phiri+ limene lili kum’mawa kwa mzindawo.+
4 Tsopano ulemerero wa Yehova+ unachoka pa akerubi n’kupita pakhomo la nyumba yopatulika, ndipo mtambo+ unadzaza nyumbayo pang’onopang’ono. Komanso ulemerero wowala wa Yehova unadzaza m’bwalo lonse la nyumbayo.
23 Kenako, ulemerero wa Yehova+ unakwera m’mwamba kuchoka pakati pa mzindawo, n’kukaima pamwamba pa phiri+ limene lili kum’mawa kwa mzindawo.+