2 Mafumu 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+ 2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Yeremiya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+
21 Mfumu ya Babuloyo inapha anthuwo+ ku Ribila m’dziko la Hamati.+ Choncho Ayuda anachoka kudziko lawo n’kupita ku ukapolo.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+