Yobu 37:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amuna inu mvetserani mwatcheru kugunda kwa mawu a Mulungu,+Ndi kubangula kochokera m’kamwa mwake. Salimo 29:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+ Salimo 68:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+
3 Liwu la Yehova lili pamwamba pa madzi,*+Liwu la Mulungu waulemerero+ lagunda ngati bingu.+Yehova ali pamwamba pa madzi ambiri.+
33 Imbirani Iye wokwera kumwamba kwa kumwamba kwakale.+Tamverani! Iye akulankhula ndi mawu amphamvu.+