Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Danieli 2:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Mfumuyo inauza Danieli kuti: “Ndithudi Mulungu wa anthu inu ndi Mulungu wa milungu yonse,+ Ambuye wa mafumu onse+ ndiponso Woulula zinsinsi, chifukwa iwe wakwanitsa kuulula chinsinsi chimenechi.”+

  • Danieli 4:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Kenako Danieli, amene ndinamupatsa dzina lakuti Belitesazara+ pofuna kulemekeza mulungu wanga,+ amenenso mwa iye muli mzimu wa milungu yoyera,+ anabwera kwa ine ndipo ndinamuuza malotowo. Ndinati:

  • Danieli 4:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “‘Amenewa ndiwo maloto amene ine Mfumu Nebukadinezara ndinalota. Tsopano iwe Belitesazara umasulire malotowa, pakuti amuna ena onse anzeru a mu ufumu wanga alephera kuwamasulira.+ Koma iwe ungathe kuwamasulira chifukwa mzimu wa milungu yoyera uli mwa iwe.’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena