Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 37:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Chipulumutso cha anthu olungama chimachokera kwa Yehova.+

      Iye ndi malo awo achitetezo champhamvu pa nthawi ya nsautso.+

  • Salimo 91:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mulungu wanena kuti: “Popeza wasonyeza kuti amandikonda,+

      Inenso ndidzamupulumutsa.+

      Ndidzamuteteza chifukwa wadziwa dzina langa.+

  • Salimo 118:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 M’masautso anga ndinaitana Ya.+

      Ya anandiyankha ndi kundiika pamalo otakasuka.+

  • Yesaya 41:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Usachite mantha, pakuti ndili nawe.+ Usayang’ane uku ndi uku mwamantha, pakuti ine ndine Mulungu wako.+ Ndikulimbitsa.+ Ndithu ndikuthandiza.+ Ndikugwira mwamphamvu ndi dzanja langa lamanja+ lachilungamo.’+

  • Yesaya 43:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ukamadzadutsa pamadzi,+ ine ndidzakhala nawe.+ Ukamadzawoloka mitsinje, madzi sadzakumiza.+ Ukamadzayenda pamoto sudzapsa ndipo ngakhale lawi la moto silidzakuwaula.+

  • 2 Akorinto 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anatipulumutsadi ku chinthu choopsa, ndicho imfa, ndipo adzatipulumutsabe.+ Tikukhulupirira kuti iye apitiriza kutipulumutsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena